
Kumasekelera munthu owononga kuti apitilile kuwononga ndi chimodzi chomwe chawononga dziko lino – Chakwera
Mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera wati dziko la Malawi likuyenera kumangidwanso pa maziko a mphamvu ndipo kusekelera anthu owononga ndi zina zomwe zasakaza maziko a dziko lino. Chakwera wati dziko la Malawi palibe chomwe lingaphule ngati …